1 Mafumu 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mfumuyo inalumbira+ kuti: “Pali Yehova+ amene anapulumutsa+ moyo wanga+ m’masautso onse,+ Salimo 34:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mngelo wa Yehova amamanga msasa mozungulira onse oopa Mulungu,+Ndipo amawapulumutsa.+