Salimo 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mawu a pakamwa panga ndi kusinkhasinkha kwa mtima wanga,+Zikukondweretseni, inu Yehova, Thanthwe langa+ ndi Wondiwombola.+ Salimo 31:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndikuikiza mzimu* wanga m’manja mwanu.+Mwandiwombola,+ inu Yehova, Mulungu wachoonadi.+ Salimo 103:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamanda amene akuwombola moyo wako kudzenje,+Amene akukuveka kukoma mtima kosatha ndi chifundo ngati chisoti chachifumu,+
14 Mawu a pakamwa panga ndi kusinkhasinkha kwa mtima wanga,+Zikukondweretseni, inu Yehova, Thanthwe langa+ ndi Wondiwombola.+
4 Tamanda amene akuwombola moyo wako kudzenje,+Amene akukuveka kukoma mtima kosatha ndi chifundo ngati chisoti chachifumu,+