Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 49:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Pakamwa panga padzalankhula zinthu zanzeru,+

      Ndipo zosinkhasinkha za mtima wanga zidzakhala zinthu zakuya.+

  • Salimo 51:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Inu Yehova, tsegulani milomo yangayi,+

      Kuti pakamwa panga patamande inu.+

  • Salimo 77:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndidzasinkhasinkha za ntchito zanu zonse,+

      Ndipo ndiziganizira zochita zanu.+

  • Salimo 143:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Ndakumbukira masiku akale.+

      Ndasinkhasinkha zochita zanu zonse,+

      Ndipo ndakhala ndikuganizira ntchito ya manja anu ndi mtima wonse.+

  • Afilipi 4:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Chomalizira abale, zinthu zilizonse zoona, zilizonse zofunika kwambiri, zilizonse zolungama, zilizonse zoyera,+ zilizonse zachikondi, zilizonse zoyamikirika, khalidwe labwino lililonse, ndi chilichonse chotamandika, pitirizani kuganizira zimenezi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena