Agalatiya 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma makhalidwe* amene mzimu woyera umatulutsa+ ndiwo chikondi, chimwemwe, mtendere, kuleza mtima, kukoma mtima, ubwino,+ chikhulupiriro, Akolose 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ikani maganizo anu pa zinthu zakumwamba,+ osati pa zinthu zapadziko.+
22 Koma makhalidwe* amene mzimu woyera umatulutsa+ ndiwo chikondi, chimwemwe, mtendere, kuleza mtima, kukoma mtima, ubwino,+ chikhulupiriro,