Yohane 3:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Wochokera kumwamba ali woposa ena onse.+ Wochokera padziko lapansi ndi wa padziko lapansi, ndipo amalankhula zinthu za padziko lapansi.+ Koma wochokera kumwamba ali woposa ena onse.+ 1 Yohane 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Musamakonde dziko kapena zinthu za m’dziko.+ Ngati wina akukonda dziko, ndiye kuti sakonda Atate.+
31 Wochokera kumwamba ali woposa ena onse.+ Wochokera padziko lapansi ndi wa padziko lapansi, ndipo amalankhula zinthu za padziko lapansi.+ Koma wochokera kumwamba ali woposa ena onse.+
15 Musamakonde dziko kapena zinthu za m’dziko.+ Ngati wina akukonda dziko, ndiye kuti sakonda Atate.+