Aroma 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Musamatengere+ nzeru za nthawi* ino, koma sandulikani mwa kusintha maganizo anu,+ kuti muzindikire+ chimene chili chifuniro+ cha Mulungu, chabwino, chovomerezeka ndi changwiro. 1 Akorinto 7:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Amene amagwiritsira ntchito dzikoli+ azikhala ngati amene sakuligwiritsira ntchito mokwanira, pakuti zochitika za padzikoli zikusintha.+ Aefeso 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho samalani kwambiri kuti mmene mukuyendera+ si monga anthu opanda nzeru, koma ngati anzeru.
2 Musamatengere+ nzeru za nthawi* ino, koma sandulikani mwa kusintha maganizo anu,+ kuti muzindikire+ chimene chili chifuniro+ cha Mulungu, chabwino, chovomerezeka ndi changwiro.
31 Amene amagwiritsira ntchito dzikoli+ azikhala ngati amene sakuligwiritsira ntchito mokwanira, pakuti zochitika za padzikoli zikusintha.+