Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Akorinto 11:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Koma nkhawa yanga ndi yakuti mwina, monga mmene njoka inanamizira Hava+ ndi chinyengo chake, maganizo anunso angapotozedwe+ kuti musakhalenso oona mtima ndi oyera ngati mmene muyenera kuchitira kwa Khristu.+

  • 1 Timoteyo 4:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Usalole kuti munthu aliyense akuderere poona kuti ndiwe wamng’ono.+ M’malomwake, ukhale chitsanzo+ kwa okhulupirika+ m’kalankhulidwe, m’makhalidwe, m’chikondi, m’chikhulupiriro, ndi pa khalidwe loyera.+

  • 1 Timoteyo 5:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 ndipo akazi achikulire+ ngati amayi ako. Akazi achitsikana uwadandaulire ngati alongo ako,+ ndipo pochita zimenezi usakhale ndi maganizo alionse oipa.

  • 1 Petulo 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 poona okha ndi maso awo khalidwe lanu loyera+ ndi ulemu wanu waukulu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena