Salimo 71:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndikafuna kuimba nyimbo zokutamandani, pakamwa panga padzafuula mokondwera,+Ngakhalenso moyo wanga umene mwauwombola+ udzakutamandani.
23 Ndikafuna kuimba nyimbo zokutamandani, pakamwa panga padzafuula mokondwera,+Ngakhalenso moyo wanga umene mwauwombola+ udzakutamandani.