Salimo 63:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Moyo wanga wakhutira ndi gawo labwino kwambiri, wakhutira ndi zinthu zabwino kwambiri,+Ndipo milomo yanga ikukutamandani ndi mfuu yachisangalalo.+ Salimo 104:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndidzaimbira Yehova moyo wanga wonse.+Ndidzaimba nyimbo zotamanda Mulungu wanga nthawi yonse ya moyo wanga.+
5 Moyo wanga wakhutira ndi gawo labwino kwambiri, wakhutira ndi zinthu zabwino kwambiri,+Ndipo milomo yanga ikukutamandani ndi mfuu yachisangalalo.+
33 Ndidzaimbira Yehova moyo wanga wonse.+Ndidzaimba nyimbo zotamanda Mulungu wanga nthawi yonse ya moyo wanga.+