Levitiko 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pakuti aliyense wodya mafuta a nyama imene waipereka kwa Yehova monga nsembe yotentha ndi moto, munthu ameneyo aziphedwa+ kuti asakhalenso pakati pa anthu a mtundu wake. Salimo 36:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Amadya ndi kukhuta chakudya chonona m’nyumba mwanu.+Ndipo mumawamwetsa mumtsinje wa zosangalatsa zanu zambiri.+ Yeremiya 31:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ansembe ndidzawatsitsimutsa ndi chakudya chochuluka,+ ndipo anthu anga ndidzawakhutiritsa ndi ubwino wanga,”+ watero Yehova.
25 Pakuti aliyense wodya mafuta a nyama imene waipereka kwa Yehova monga nsembe yotentha ndi moto, munthu ameneyo aziphedwa+ kuti asakhalenso pakati pa anthu a mtundu wake.
8 Amadya ndi kukhuta chakudya chonona m’nyumba mwanu.+Ndipo mumawamwetsa mumtsinje wa zosangalatsa zanu zambiri.+
14 Ansembe ndidzawatsitsimutsa ndi chakudya chochuluka,+ ndipo anthu anga ndidzawakhutiritsa ndi ubwino wanga,”+ watero Yehova.