Salimo 65:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Wodala ndi munthu amene inu mwamusankha ndi kumuyandikizitsa kwa inu,+Kuti akhale m’mabwalo anu.+Tidzakhutira ndi zinthu zabwino za m’nyumba yanu,+Malo anu oyera kapena kuti kachisi wanu woyera.+ Yeremiya 31:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ansembe ndidzawatsitsimutsa ndi chakudya chochuluka,+ ndipo anthu anga ndidzawakhutiritsa ndi ubwino wanga,”+ watero Yehova. Zekariya 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ubwino wake ndi waukulu kwambiri+ ndiponso iye ndi wooneka bwino kwambiri.+ Tirigu adzapatsa mphamvu anyamata ndipo vinyo watsopano adzapatsa mphamvu anamwali.”+
4 Wodala ndi munthu amene inu mwamusankha ndi kumuyandikizitsa kwa inu,+Kuti akhale m’mabwalo anu.+Tidzakhutira ndi zinthu zabwino za m’nyumba yanu,+Malo anu oyera kapena kuti kachisi wanu woyera.+
14 Ansembe ndidzawatsitsimutsa ndi chakudya chochuluka,+ ndipo anthu anga ndidzawakhutiritsa ndi ubwino wanga,”+ watero Yehova.
17 Ubwino wake ndi waukulu kwambiri+ ndiponso iye ndi wooneka bwino kwambiri.+ Tirigu adzapatsa mphamvu anyamata ndipo vinyo watsopano adzapatsa mphamvu anamwali.”+