Yesaya 62:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova walumbira ndi dzanja lake lamanja+ ndiponso ndi mkono wake wamphamvu+ kuti: “Sindidzaperekanso mbewu zanu kwa adani anu ngati chakudya,+ ndipo alendo sadzamwanso vinyo wanu watsopano+ amene munachita kumuvutikira. Yoweli 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Nthawi imeneyo mapiri adzachucha vinyo wotsekemera.+ Mkaka udzayenda pazitunda ndipo m’mitsinje yonse ya Yuda mudzayenda madzi. Kasupe wamadzi adzatuluka m’nyumba ya Yehova+ ndi kuthirira chigwa cha Mitengo ya Mthethe.+ Amosi 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Yehova wanena kuti, ‘Masiku adzafika pamene wolima adzapitirira wokolola,+ ndipo woponda mphesa adzapitirira munthu amene wanyamula mbewu zoti akabzale.+ Mapiri adzachucha vinyo wotsekemera*+ ndipo zitunda zonse zidzatulutsa vinyo wochuluka.+
8 Yehova walumbira ndi dzanja lake lamanja+ ndiponso ndi mkono wake wamphamvu+ kuti: “Sindidzaperekanso mbewu zanu kwa adani anu ngati chakudya,+ ndipo alendo sadzamwanso vinyo wanu watsopano+ amene munachita kumuvutikira.
18 “Nthawi imeneyo mapiri adzachucha vinyo wotsekemera.+ Mkaka udzayenda pazitunda ndipo m’mitsinje yonse ya Yuda mudzayenda madzi. Kasupe wamadzi adzatuluka m’nyumba ya Yehova+ ndi kuthirira chigwa cha Mitengo ya Mthethe.+
13 “Yehova wanena kuti, ‘Masiku adzafika pamene wolima adzapitirira wokolola,+ ndipo woponda mphesa adzapitirira munthu amene wanyamula mbewu zoti akabzale.+ Mapiri adzachucha vinyo wotsekemera*+ ndipo zitunda zonse zidzatulutsa vinyo wochuluka.+