Levitiko 26:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamenepo, mudzakhala mukupuntha zimene mwakolola kufikira nyengo yokolola mphesa, ndipo mudzakhala mukukolola mphesa kufikira nyengo yofesa mbewu. Mudzadya mkate wanu ndi kukhuta,+ ndipo mudzakhala otetezeka m’dziko lanu.+ Ezekieli 36:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Anthu adzanena kuti: “Dziko ilo limene linali bwinja tsopano lakhala ngati munda wa Edeni.+ Mizinda imene inawonongedwa ija, imene inali mabwinja ndiponso imene nyumba zake zinagwetsedwa, tsopano ili ndi mipanda yolimba kwambiri ndipo mukukhala anthu.”+
5 Pamenepo, mudzakhala mukupuntha zimene mwakolola kufikira nyengo yokolola mphesa, ndipo mudzakhala mukukolola mphesa kufikira nyengo yofesa mbewu. Mudzadya mkate wanu ndi kukhuta,+ ndipo mudzakhala otetezeka m’dziko lanu.+
35 Anthu adzanena kuti: “Dziko ilo limene linali bwinja tsopano lakhala ngati munda wa Edeni.+ Mizinda imene inawonongedwa ija, imene inali mabwinja ndiponso imene nyumba zake zinagwetsedwa, tsopano ili ndi mipanda yolimba kwambiri ndipo mukukhala anthu.”+