Amosi 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Yehova wanena kuti, ‘Masiku adzafika pamene wolima adzapitirira wokolola,+ ndipo woponda mphesa adzapitirira munthu amene wanyamula mbewu zoti akabzale.+ Mapiri adzachucha vinyo wotsekemera*+ ndipo zitunda zonse zidzatulutsa vinyo wochuluka.+ Zekariya 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ubwino wake ndi waukulu kwambiri+ ndiponso iye ndi wooneka bwino kwambiri.+ Tirigu adzapatsa mphamvu anyamata ndipo vinyo watsopano adzapatsa mphamvu anamwali.”+
13 “Yehova wanena kuti, ‘Masiku adzafika pamene wolima adzapitirira wokolola,+ ndipo woponda mphesa adzapitirira munthu amene wanyamula mbewu zoti akabzale.+ Mapiri adzachucha vinyo wotsekemera*+ ndipo zitunda zonse zidzatulutsa vinyo wochuluka.+
17 Ubwino wake ndi waukulu kwambiri+ ndiponso iye ndi wooneka bwino kwambiri.+ Tirigu adzapatsa mphamvu anyamata ndipo vinyo watsopano adzapatsa mphamvu anamwali.”+