Yoweli 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Nthawi imeneyo mapiri adzachucha vinyo wotsekemera.+ Mkaka udzayenda pazitunda ndipo m’mitsinje yonse ya Yuda mudzayenda madzi. Kasupe wamadzi adzatuluka m’nyumba ya Yehova+ ndi kuthirira chigwa cha Mitengo ya Mthethe.+
18 “Nthawi imeneyo mapiri adzachucha vinyo wotsekemera.+ Mkaka udzayenda pazitunda ndipo m’mitsinje yonse ya Yuda mudzayenda madzi. Kasupe wamadzi adzatuluka m’nyumba ya Yehova+ ndi kuthirira chigwa cha Mitengo ya Mthethe.+