Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 46:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Pali mtsinje womwe nthambi zake zimachititsa anthu a mumzinda wa Mulungu kukondwera,+

      Chihema chachikulu chopatulika koposa cha Wam’mwambamwamba.+

  • Ezekieli 47:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Kenako ananditenga n’kupita nanenso kukhomo la Nyumbayo.+ Kumeneko ndinaona madzi+ akutuluka pansi, pakhomo penipeni pa Nyumbayo chakum’mawa,+ pakuti Nyumbayo inayang’ana kum’mawa. Madziwo anali kutuluka pansi n’kumatsetsereka. Anali kutuluka kuchokera kumbali ya kudzanja lamanja kwa Nyumbayo, n’kudutsa kum’mwera kwa guwa lansembe.

  • Chivumbulutso 22:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndipo anandionetsa mtsinje wa madzi a moyo,+ oyera ngati mwala wonyezimira wa kulusitalo, ukuyenda kuchokera kumpando wachifumu wa Mulungu, ndi wa Mwanawankhosa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena