Yeremiya 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 ‘chifukwa pali zinthu ziwiri zoipa zimene anthu anga achita: Iwo asiya ine+ kasupe wa madzi amoyo,+ ndipo akumba zitsime zawozawo, zitsime zong’ambika zimene sizingasunge madzi.’ Zekariya 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Pa tsiku limenelo,+ kudzakumbidwa chitsime+ kuti a m’nyumba ya Davide ndi anthu okhala mu Yerusalemu adzayeretsedwe ku machimo+ ndi ku zinthu zawo zonyansa.+ Zekariya 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pa tsiku limenelo madzi amoyo+ adzatuluka mu Yerusalemu.+ Hafu ya madziwo idzapita kunyanja ya kum’mawa+ ndipo hafu inayo idzapita kunyanja ya kumadzulo.+ Zimenezi zidzachitika m’chilimwe ndiponso m’nyengo yozizira.+
13 ‘chifukwa pali zinthu ziwiri zoipa zimene anthu anga achita: Iwo asiya ine+ kasupe wa madzi amoyo,+ ndipo akumba zitsime zawozawo, zitsime zong’ambika zimene sizingasunge madzi.’
13 “Pa tsiku limenelo,+ kudzakumbidwa chitsime+ kuti a m’nyumba ya Davide ndi anthu okhala mu Yerusalemu adzayeretsedwe ku machimo+ ndi ku zinthu zawo zonyansa.+
8 Pa tsiku limenelo madzi amoyo+ adzatuluka mu Yerusalemu.+ Hafu ya madziwo idzapita kunyanja ya kum’mawa+ ndipo hafu inayo idzapita kunyanja ya kumadzulo.+ Zimenezi zidzachitika m’chilimwe ndiponso m’nyengo yozizira.+