Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Kuyambira kuphazi mpaka kumutu palibe pabwino.+ Thupi lanu lonse lili ndi mabala ndi zilonda, ndiponso lanyukanyuka. Palibe amene wafinya zilonda zanuzo kapena kuzimanga. Palibenso amene wazifewetsa ndi mafuta.+

  • Ezekieli 36:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ine ndidzakuwazani madzi oyera ndipo mudzakhala oyera. Ndidzakuyeretsani+ pokuchotserani zonyansa zanu zonse+ ndi mafano anu onse onyansa.+

  • Yohane 1:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Tsiku lotsatira anaona Yesu akubwera kwa iye, ndipo anati: “Taonani, Mwanawankhosa+ wa Mulungu amene akuchotsa uchimo+ wa dziko!+

  • Machitidwe 2:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Petulo anawayankha kuti: “Lapani,+ ndipo aliyense wa inu abatizidwe+ m’dzina+ la Yesu Khristu kuti machimo anu akhululukidwe.+ Mukatero mudzalandira mphatso yaulere+ ya mzimu woyera.

  • Machitidwe 2:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Choncho amene analandira mawu akewo ndi mtima wonse anabatizidwa,+ moti tsiku limenelo chiwerengero cha ophunzirawo chinawonjezeka ndi anthu pafupifupi 3,000.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena