Luka 24:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 ndipo pa maziko a dzina lake, m’mitundu yonse+ mudzalalikidwa za kulapa kuti machimo akhululukidwe.+ Kuyambira ku Yerusalemu+ Machitidwe 17:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Zoona, Mulungu analekerera nthawi ya kusadziwa koteroko,+ koma tsopano akuuza anthu kwina kulikonse kuti onse alape.+ Machitidwe 26:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma kuyambira kwa okhala ku Damasiko+ ndi ku Yerusalemu,+ komanso m’dziko lonse la Yudeya ndi kwa anthu a mitundu ina,+ ndinafikitsa uthenga wakuti alape ndi kutembenukira kwa Mulungu mwa kuchita ntchito zosonyeza kulapa.+
47 ndipo pa maziko a dzina lake, m’mitundu yonse+ mudzalalikidwa za kulapa kuti machimo akhululukidwe.+ Kuyambira ku Yerusalemu+
30 Zoona, Mulungu analekerera nthawi ya kusadziwa koteroko,+ koma tsopano akuuza anthu kwina kulikonse kuti onse alape.+
20 Koma kuyambira kwa okhala ku Damasiko+ ndi ku Yerusalemu,+ komanso m’dziko lonse la Yudeya ndi kwa anthu a mitundu ina,+ ndinafikitsa uthenga wakuti alape ndi kutembenukira kwa Mulungu mwa kuchita ntchito zosonyeza kulapa.+