Machitidwe 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Saulo anapitiriza kupeza mphamvu zambiri, ndipo anali kuthetsa nzeru Ayuda okhala mu Damasiko powafotokozera mfundo zomveka zotsimikizira kuti Yesu ndiyedi Khristu.+
22 Koma Saulo anapitiriza kupeza mphamvu zambiri, ndipo anali kuthetsa nzeru Ayuda okhala mu Damasiko powafotokozera mfundo zomveka zotsimikizira kuti Yesu ndiyedi Khristu.+