Machitidwe 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Komabe Saulo anapitiriza kukhala ndi mphamvu zambiri ndipo ankathetsa nzeru Ayuda a ku Damasiko powafotokozera mfundo zomveka zotsimikizira kuti Yesu ndi Khristu.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:22 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 64 Sukulu ya Utumiki, tsa. 170
22 Komabe Saulo anapitiriza kukhala ndi mphamvu zambiri ndipo ankathetsa nzeru Ayuda a ku Damasiko powafotokozera mfundo zomveka zotsimikizira kuti Yesu ndi Khristu.+