Machitidwe 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye anali kufotokoza ndi kusonyeza umboni wolembedwa powatsimikizira kuti kunali koyenera kuti Khristu avutike+ ndi kuuka kwa akufa.+ Anali kunena kuti: “Yesu amene ndikumulalikira kwa inu, ndiye Khristu.”+ Machitidwe 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pakuti mwamphamvu, iye anawatsimikizira Ayuda poyera kuti anali olakwa, ndipo anasonyeza mwa Malemba+ kuti Yesu ndiyedi Khristu.+
3 Iye anali kufotokoza ndi kusonyeza umboni wolembedwa powatsimikizira kuti kunali koyenera kuti Khristu avutike+ ndi kuuka kwa akufa.+ Anali kunena kuti: “Yesu amene ndikumulalikira kwa inu, ndiye Khristu.”+
28 Pakuti mwamphamvu, iye anawatsimikizira Ayuda poyera kuti anali olakwa, ndipo anasonyeza mwa Malemba+ kuti Yesu ndiyedi Khristu.+