Machitidwe 5:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ameneyo Mulungu anamukweza kudzanja lake lamanja+ monga Mtumiki Wamkulu+ ndi Mpulumutsi.+ Anachita zimenezi kuti Aisiraeli alape+ ndi kuti machimo awo akhululukidwe.+ Machitidwe 13:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 “Chotero dziwani abale anga kuti, ife tikulalikira kwa inu za kukhululukidwa kwa machimo kudzera mwa Iyeyu.+
31 Ameneyo Mulungu anamukweza kudzanja lake lamanja+ monga Mtumiki Wamkulu+ ndi Mpulumutsi.+ Anachita zimenezi kuti Aisiraeli alape+ ndi kuti machimo awo akhululukidwe.+
38 “Chotero dziwani abale anga kuti, ife tikulalikira kwa inu za kukhululukidwa kwa machimo kudzera mwa Iyeyu.+