Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 29:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndiyeno anawauza kuti: “Tamverani Alevi inu. Dziyeretseni+ ndipo muyeretsenso nyumba ya Yehova Mulungu wa makolo anu. Mutulutse chinthu chodetsedwa m’malo oyera.+

  • Maliro 1:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Yerusalemu wachita tchimo+ lalikulu. N’chifukwa chake wakhala chinthu chonyansa.+

      Onse amene anali kumulemekeza ayamba kumuona ngati chinthu chachabechabe,+ chifukwa aona maliseche+ ake.

      Iyenso akuusa moyo+ ndipo watembenukira kwina chifukwa cha manyazi.

  • Ezekieli 36:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Iwe mwana wa munthu, pamene a nyumba ya Isiraeli anali kukhala m’dziko lawo, anali kudetsa dzikolo ndi njira zawo komanso zochita zawo.+ Pamaso panga, njira zawo zakhala ngati zonyansa za mkazi amene akusamba.+

  • Ezekieli 36:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 “‘Ndidzakupulumutsani ku zinthu zanu zonse zodetsa,+ ndipo ndidzauza mbewu kuti zibereke kwambiri moti sindidzabweretsanso njala pakati panu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena