Ekisodo 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako anauza anthuwo kuti: “Pofika tsiku lachitatu mukhale okonzeka.+ Amunanu musayandikire akazi anu.”*+ 1 Mbiri 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano Davide anawauza kuti: “Inuyo ndinu atsogoleri+ a nyumba ya makolo a Alevi. Choncho inu ndi abale anu mudziyeretse,+ ndipo mukatenge likasa la Yehova Mulungu wa Isiraeli n’kukaliika kumalo amene ine ndakonza kuti likakhaleko.
15 Kenako anauza anthuwo kuti: “Pofika tsiku lachitatu mukhale okonzeka.+ Amunanu musayandikire akazi anu.”*+
12 Tsopano Davide anawauza kuti: “Inuyo ndinu atsogoleri+ a nyumba ya makolo a Alevi. Choncho inu ndi abale anu mudziyeretse,+ ndipo mukatenge likasa la Yehova Mulungu wa Isiraeli n’kukaliika kumalo amene ine ndakonza kuti likakhaleko.