1 Samueli 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotero amuna a ku Kiriyati-yearimu+ anabweradi ndi kutenga likasa la Yehova n’kupita nalo kwawo, ndipo analiika m’nyumba ya Abinadabu+ imene inali paphiri. Anapatula Eleazara mwana wake kuti azilondera likasa la Yehova.
7 Chotero amuna a ku Kiriyati-yearimu+ anabweradi ndi kutenga likasa la Yehova n’kupita nalo kwawo, ndipo analiika m’nyumba ya Abinadabu+ imene inali paphiri. Anapatula Eleazara mwana wake kuti azilondera likasa la Yehova.