-
2 Samueli 6:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Choncho ananyamula likasa la Mulungu woona kulichotsa kunyumba ya Abinadabu imene inali paphiri, ndipo Ahiyo anali kuyenda patsogolo pa Likasa.
-