2 Samueli 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma iwo anakweza likasa la Mulungu woona pangolo yatsopano+ kuti alichotse kunyumba ya Abinadabu+ imene inali paphiri. Uza ndi Ahiyo,+ ana aamuna a Abinadabu, anali kutsogolera ngolo yatsopanoyo.
3 Koma iwo anakweza likasa la Mulungu woona pangolo yatsopano+ kuti alichotse kunyumba ya Abinadabu+ imene inali paphiri. Uza ndi Ahiyo,+ ana aamuna a Abinadabu, anali kutsogolera ngolo yatsopanoyo.