Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 25:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ulowetse mitengo yonyamulirayo mumphete zija za m’mbali mwa Likasa kuti azinyamulira Likasalo.

  • Numeri 7:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma ana a Kohati sanawagawire zinthuzo, chifukwa utumiki wawo unali wonyamula zinthu za pamalo oyera,+ ndipo anali kuzinyamulira paphewa.+

  • Yoswa 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndipo zimenezi zinachitikadi. Anthuwo anachotsa mahema awo, n’kunyamuka. Anayandikira Yorodano kuti awoloke, ndipo ansembe onyamula likasa+ la pangano anali patsogolo pawo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena