2 Samueli 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano onyamula+ likasa la Yehova atangoyenda mapazi 6, nthawi yomweyo Davide anapereka nsembe ng’ombe yamphongo ndi chiweto chonenepa.+ 1 Mbiri 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno ana a Alevi anakanyamula+ likasa la Mulungu woona, monga mmene Mose anawalamulira potsatira mawu a Yehova. Iwo analinyamula pamapewa awo pogwiritsa ntchito ndodo zake.+
13 Tsopano onyamula+ likasa la Yehova atangoyenda mapazi 6, nthawi yomweyo Davide anapereka nsembe ng’ombe yamphongo ndi chiweto chonenepa.+
15 Ndiyeno ana a Alevi anakanyamula+ likasa la Mulungu woona, monga mmene Mose anawalamulira potsatira mawu a Yehova. Iwo analinyamula pamapewa awo pogwiritsa ntchito ndodo zake.+