1 Mbiri 15:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mulungu woona atathandiza+ Alevi ponyamula likasa la pangano la Yehova, iwo anapereka nsembe ng’ombe zazing’ono zamphongo 7, ndi nkhosa zamphongo 7.+
26 Mulungu woona atathandiza+ Alevi ponyamula likasa la pangano la Yehova, iwo anapereka nsembe ng’ombe zazing’ono zamphongo 7, ndi nkhosa zamphongo 7.+