2 Samueli 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano onyamula+ likasa la Yehova atangoyenda mapazi 6, nthawi yomweyo Davide anapereka nsembe ng’ombe yamphongo ndi chiweto chonenepa.+
13 Tsopano onyamula+ likasa la Yehova atangoyenda mapazi 6, nthawi yomweyo Davide anapereka nsembe ng’ombe yamphongo ndi chiweto chonenepa.+