Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 4:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Aroni ndi ana ake akamaliza kuphimba zinthu za m’malo oyera+ ndi ziwiya zonse+ za m’malo oyerawo posamutsa msasa, ana a Kohati azilowamo n’kudzazinyamula.+ Iwo asamakhudze+ zinthu za m’malo oyerazo chifukwa angafe. Zinthu zimenezi ndizo katundu wa m’chihema chokumanako amene ana a Kohati azinyamula.+

  • Numeri 7:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma ana a Kohati sanawagawire zinthuzo, chifukwa utumiki wawo unali wonyamula zinthu za pamalo oyera,+ ndipo anali kuzinyamulira paphewa.+

  • Yoswa 3:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 ndipo anauza anthuwo kuti: “Mukangoona likasa la pangano la Yehova Mulungu wanu litanyamulidwa ndi ansembe achilevi,+ musamuke pamalo panu ndi kulitsatira,

  • 1 Mbiri 15:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pa nthawi imeneyi m’pamene Davide ananena kuti: “Alevi okha ndiwo ayenera kunyamula likasa la Mulungu woona, chifukwa Yehova anasankha iwowa kuti azinyamula likasa la Yehova+ ndi kum’tumikira+ mpaka kalekale.”*

  • 1 Mbiri 15:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndiyeno ana a Alevi anakanyamula+ likasa la Mulungu woona, monga mmene Mose anawalamulira potsatira mawu a Yehova. Iwo analinyamula pamapewa awo pogwiritsa ntchito ndodo zake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena