Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 7:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma ana a Kohati sanawagawire zinthuzo, chifukwa utumiki wawo unali wonyamula zinthu za pamalo oyera,+ ndipo anali kuzinyamulira paphewa.+

  • Numeri 10:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Kenako Akohati, onyamula zinthu za m’malo opatulika+ ananyamuka, kuti pokafika akapeze chihema chopatulika chitamangidwa kale.

  • Deuteronomo 31:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pamenepo Mose analemba chilamulo chimenechi+ ndi kuchipereka kwa ansembe, ana a Levi,+ onyamula likasa la pangano la Yehova.+ Anachiperekanso kwa akulu onse a Isiraeli.

  • 1 Mbiri 15:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pa nthawi imeneyi m’pamene Davide ananena kuti: “Alevi okha ndiwo ayenera kunyamula likasa la Mulungu woona, chifukwa Yehova anasankha iwowa kuti azinyamula likasa la Yehova+ ndi kum’tumikira+ mpaka kalekale.”*

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena