Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 40:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndipo udzawadzoze ngati mmene wadzozera abambo awo+ kuti atumikire monga ansembe anga. Iwo adzatumikirabe monga ansembe odzozedwa m’mibadwo yawo yonse mpaka kalekale.”+

  • Numeri 8:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pambuyo pake, Aleviwo azitumikira pachihema chokumanako.+ Chotero uwayeretse, ndi kuwauza kuti ayende uku ndi uku monga nsembe yoweyula.+

  • Numeri 18:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Utengenso abale ako a fuko la Levi, amtundu wa bambo ako, kuti azikhala pafupi ndi inu. Azitumikira+ iweyo limodzi ndi ana ako pachihema cha Umboni.+

  • Deuteronomo 21:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Ansembe, ana a Levi, azifika pafupi chifukwa ndi amene Yehova Mulungu wanu wawasankha kuti am’tumikire+ ndi kudalitsa+ m’dzina la Yehova. Iwo ndiwo ayenera kuthetsa mkangano uliwonse wokhudza choipa chilichonse chimene chachitika.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena