Numeri 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Itanitsa fuko la Levi+ ndipo uwapereke kwa wansembe Aroni kuti azimutumikira.+ Numeri 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno Aleviwo analowa n’kukayamba utumiki wawo m’chihema chokumanako, pamaso pa Aroni ndi ana ake.+ Anthu anachitira Aleviwo malinga ndi zimene Yehova analamula Mose zokhudza Alevi. Numeri 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi amuna inu mukuyesa n’chinthu chaching’ono kuti Mulungu wa Isiraeli anakupatulani+ pakati pa Aisiraeli, n’kukutengani kukhala akeake, kuti muzitumikira Yehova pachihema chake ndi kutumikira khamulo?+
22 Ndiyeno Aleviwo analowa n’kukayamba utumiki wawo m’chihema chokumanako, pamaso pa Aroni ndi ana ake.+ Anthu anachitira Aleviwo malinga ndi zimene Yehova analamula Mose zokhudza Alevi.
9 Kodi amuna inu mukuyesa n’chinthu chaching’ono kuti Mulungu wa Isiraeli anakupatulani+ pakati pa Aisiraeli, n’kukutengani kukhala akeake, kuti muzitumikira Yehova pachihema chake ndi kutumikira khamulo?+