-
Numeri 8:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Ndiyeno Aleviwo analowa mʼchihema chokumanako nʼkukayamba utumiki wawo pamaso pa Aroni ndi ana ake. Anthu anachitira Aleviwo mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose zokhudza Alevi.
-