Numeri 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno Aleviwo analowa n’kukayamba utumiki wawo m’chihema chokumanako, pamaso pa Aroni ndi ana ake.+ Anthu anachitira Aleviwo malinga ndi zimene Yehova analamula Mose zokhudza Alevi.
22 Ndiyeno Aleviwo analowa n’kukayamba utumiki wawo m’chihema chokumanako, pamaso pa Aroni ndi ana ake.+ Anthu anachitira Aleviwo malinga ndi zimene Yehova analamula Mose zokhudza Alevi.