Numeri 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Muwerenge kuyambira azaka 30+ mpaka 50,+ onse olowa m’gulu la ogwira ntchito+ m’chihema chokumanako. Numeri 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo, Aroni auze Aleviwo kuti ayende uku ndi uku pamaso pa Yehova monga nsembe yoweyula*+ ya ana a Isiraeli. Iwo azigwira ntchito yotumikira Yehova.+
3 Muwerenge kuyambira azaka 30+ mpaka 50,+ onse olowa m’gulu la ogwira ntchito+ m’chihema chokumanako.
11 Pamenepo, Aroni auze Aleviwo kuti ayende uku ndi uku pamaso pa Yehova monga nsembe yoweyula*+ ya ana a Isiraeli. Iwo azigwira ntchito yotumikira Yehova.+