Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 7:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Iye azibweretsa mafuta+ pamodzi ndi nganga monga nsembe kwa Yehova yotentha ndi moto. Azibweretsa mafutawo pamodzi ndi nganga kuti aziweyule* uku ndi uku, monga nsembe yoweyula+ yoperekedwa kwa Yehova.

  • Levitiko 8:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Atatero anaika zonsezi m’manja mwa Aroni ndi m’manja mwa ana ake n’kuyamba kuziweyula* uku ndi uku monga nsembe yoweyula yoperekedwa kwa Yehova.+

  • Numeri 8:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Aleviwo anadziyeretsa+ n’kuchapa zovala zawo. Pambuyo pake, Aroni anawauza kuti ayende uku ndi uku monga nsembe yoweyula pamaso pa Yehova.+ Kenako Aroniyo anawaphimbira machimo awo kuti awayeretse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena