Numeri 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo, Aroni auze Aleviwo kuti ayende uku ndi uku pamaso pa Yehova monga nsembe yoweyula*+ ya ana a Isiraeli. Iwo azigwira ntchito yotumikira Yehova.+
11 Pamenepo, Aroni auze Aleviwo kuti ayende uku ndi uku pamaso pa Yehova monga nsembe yoweyula*+ ya ana a Isiraeli. Iwo azigwira ntchito yotumikira Yehova.+