Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 1:50
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 Iweyo uike Aleviwo kukhala oyang’anira chihema cha Umboni+ ndi ziwiya zake zonse, ndi chilichonse cha mmenemo.+ Iwowo ndi amene azinyamula chihema chopatulikacho ndi ziwiya zake zonse.+ Ndi amenenso azitumikira+ pachihemapo, ndipo azimanga misasa yawo mochizungulira.+

  • Numeri 3:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Itanitsa fuko la Levi+ ndipo uwapereke kwa wansembe Aroni kuti azimutumikira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena