Ekisodo 38:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano izi ndiye zinthu zonse zimene anawerengera za chihema chopatulika, chihema cha Umboni,+ monga mwa ntchito ya Alevi,+ motsogoleredwa ndi Itamara+ mwana wa Aroni wansembe. Iwo anawerengera zimenezi Mose atalamula. Numeri 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Azisamalira ziwiya zonse+ za pachihema chokumanako, monga gawo limodzi la ntchito za ana a Isiraeli zimene a fuko la Leviwo aziwagwirira potumikira pachihema chopatulika.+
21 Tsopano izi ndiye zinthu zonse zimene anawerengera za chihema chopatulika, chihema cha Umboni,+ monga mwa ntchito ya Alevi,+ motsogoleredwa ndi Itamara+ mwana wa Aroni wansembe. Iwo anawerengera zimenezi Mose atalamula.
8 Azisamalira ziwiya zonse+ za pachihema chokumanako, monga gawo limodzi la ntchito za ana a Isiraeli zimene a fuko la Leviwo aziwagwirira potumikira pachihema chopatulika.+