Ekisodo 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Aroni anatenga Eliseba, mwana wamkazi wa Aminadabu, mlongo wake wa Naasoni,+ kukhala mkazi wake. Ndipo Eliseba anam’berekera Nadabu, Abihu, Eleazara ndi Itamara.+ Numeri 4:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Uwu ndiwo utumiki umene mabanja a ana a Gerisoni+ azichita m’chihema chokumanako. Itamara+ mwana wa wansembe Aroni, ndiye aziyang’anira utumiki wawo. 1 Mbiri 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ana a Amuramu+ anali Aroni,+ Mose,+ ndi Miriamu.+ Ana a Aroni anali Nadabu,+ Abihu,+ Eleazara,+ ndi Itamara.+
23 Aroni anatenga Eliseba, mwana wamkazi wa Aminadabu, mlongo wake wa Naasoni,+ kukhala mkazi wake. Ndipo Eliseba anam’berekera Nadabu, Abihu, Eleazara ndi Itamara.+
28 Uwu ndiwo utumiki umene mabanja a ana a Gerisoni+ azichita m’chihema chokumanako. Itamara+ mwana wa wansembe Aroni, ndiye aziyang’anira utumiki wawo.
3 Ana a Amuramu+ anali Aroni,+ Mose,+ ndi Miriamu.+ Ana a Aroni anali Nadabu,+ Abihu,+ Eleazara,+ ndi Itamara.+