Ekisodo 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Koma iwe patula Aroni m’bale wako pamodzi ndi ana ake pakati pa ana a Isiraeli, ndipo Aroniyo+ atumikire monga wansembe wanga pamodzi ndi ana akewo,+ Nadabu, Abihu,+ Eleazara ndi Itamara.+ 1 Mbiri 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Nadabu ndi Abihu+ anamwalira opanda ana aamuna bambo awo akali ndi moyo,+ koma Eleazara+ ndi Itamara anapitiriza kukhala ansembe.
28 “Koma iwe patula Aroni m’bale wako pamodzi ndi ana ake pakati pa ana a Isiraeli, ndipo Aroniyo+ atumikire monga wansembe wanga pamodzi ndi ana akewo,+ Nadabu, Abihu,+ Eleazara ndi Itamara.+
2 Nadabu ndi Abihu+ anamwalira opanda ana aamuna bambo awo akali ndi moyo,+ koma Eleazara+ ndi Itamara anapitiriza kukhala ansembe.