Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 38:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Tsopano izi ndiye zinthu zonse zimene anawerengera za chihema chopatulika, chihema cha Umboni,+ monga mwa ntchito ya Alevi,+ motsogoleredwa ndi Itamara+ mwana wa Aroni wansembe. Iwo anawerengera zimenezi Mose atalamula.

  • Levitiko 10:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndiyeno Mose anafunafuna mbuzi ya nsembe yamachimo,+ koma anaona kuti yonse inali itatenthedwa pamoto. Pamenepo iye anakwiyira Eleazara ndi Itamara, ana a Aroni amene anatsala, ndipo anati:

  • 1 Mbiri 6:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ana a Amuramu+ anali Aroni,+ Mose,+ ndi Miriamu.+ Ana a Aroni anali Nadabu,+ Abihu,+ Eleazara,+ ndi Itamara.+

  • 1 Mbiri 24:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Nadabu ndi Abihu+ anamwalira opanda ana aamuna bambo awo akali ndi moyo,+ koma Eleazara+ ndi Itamara anapitiriza kukhala ansembe.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena