Ekisodo 25:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 M’Likasamo uikemo umboni umene ndidzakupatsa.+ Ekisodo 31:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno atamaliza kulankhula naye paphiri la Sinai, anapatsa Mose miyala iwiri yosema ya Umboni,+ miyala yolembedwapo mawu ndi chala cha Mulungu.+ Ekisodo 34:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno Mose anatsika m’phiri la Sinai atanyamula miyala iwiri ija ya Umboni m’manja mwake,+ koma iye sanadziwe kuti nkhope yake inali kuwala chifukwa anali atalankhula ndi Mulungu.+ Numeri 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Mose anakaika ndodozo pamaso pa Yehova m’chihema cha Umboni.+
18 Ndiyeno atamaliza kulankhula naye paphiri la Sinai, anapatsa Mose miyala iwiri yosema ya Umboni,+ miyala yolembedwapo mawu ndi chala cha Mulungu.+
29 Ndiyeno Mose anatsika m’phiri la Sinai atanyamula miyala iwiri ija ya Umboni m’manja mwake,+ koma iye sanadziwe kuti nkhope yake inali kuwala chifukwa anali atalankhula ndi Mulungu.+