Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 8:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ataona zimenezi ansembe ochita zamatsenga anauza Farao kuti: “Chimenechi ndi chala cha Mulungu!”+ Koma Farao anapitiriza kuumitsa mtima wake,+ ndipo sanamvere, monga momwe Yehova ananenera.

  • Mateyu 12:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Koma ngati ine ndimatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya mzimu wa Mulungu, ndiye kuti ufumu wa Mulungu wakufikani modzidzimutsa.+

  • Luka 11:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Koma ngati ziwandazo ndikuzitulutsa ndi chala cha Mulungu,+ ndiye kuti ufumu wa Mulungu wakufikiranidi modzidzimutsa.+

  • 2 Akorinto 3:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pakuti zikuonekeratu kuti ndinu kalata yochokera kwa Khristu yolembedwa ndi ifeyo kudzera mu utumiki wathu.+ Kalatayo siyolembedwa ndi inki koma ndi mzimu+ wa Mulungu wamoyo. Siyolembedwa pazolembapo zamiyala,+ koma zamnofu, pamitima.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena