Ekisodo 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ataona zimenezi ansembe ochita zamatsenga anauza Farao kuti: “Chimenechi ndi chala cha Mulungu!”+ Koma Farao anapitiriza kuumitsa mtima wake,+ ndipo sanamvere, monga momwe Yehova ananenera. Mateyu 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma ngati ine ndimatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya mzimu wa Mulungu, ndiye kuti ufumu wa Mulungu wakufikani modzidzimutsa.+
19 Ataona zimenezi ansembe ochita zamatsenga anauza Farao kuti: “Chimenechi ndi chala cha Mulungu!”+ Koma Farao anapitiriza kuumitsa mtima wake,+ ndipo sanamvere, monga momwe Yehova ananenera.
28 Koma ngati ine ndimatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya mzimu wa Mulungu, ndiye kuti ufumu wa Mulungu wakufikani modzidzimutsa.+