Ekisodo 38:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano izi ndiye zinthu zonse zimene anawerengera za chihema chopatulika, chihema cha Umboni,+ monga mwa ntchito ya Alevi,+ motsogoleredwa ndi Itamara+ mwana wa Aroni wansembe. Iwo anawerengera zimenezi Mose atalamula. Numeri 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndodozo uziike m’chihema chokumanako, patsogolo pa Umboni,+ pamene ndimakumana nawe nthawi zonse.+ Numeri 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Utengenso abale ako a fuko la Levi, amtundu wa bambo ako, kuti azikhala pafupi ndi inu. Azitumikira+ iweyo limodzi ndi ana ako pachihema cha Umboni.+
21 Tsopano izi ndiye zinthu zonse zimene anawerengera za chihema chopatulika, chihema cha Umboni,+ monga mwa ntchito ya Alevi,+ motsogoleredwa ndi Itamara+ mwana wa Aroni wansembe. Iwo anawerengera zimenezi Mose atalamula.
2 Utengenso abale ako a fuko la Levi, amtundu wa bambo ako, kuti azikhala pafupi ndi inu. Azitumikira+ iweyo limodzi ndi ana ako pachihema cha Umboni.+